Ufulu wa alimi potsunga mbewu: Zochitika dziko la Guatemala
Uploaded 7 years ago | Loading

14:00
Ife alimi, abambo ndi amai, tili ndi ufulu ogulitsa mbeu zathu, kutsunga komaso kusithana. Ngati atiletsa kutsasa malonda kapena kugulitsa mbeu ya mbatata, izi ziika moyo wathu pachiopsezo, chifukwa ndi zomwe timadalira.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight