Kuumitsa Matsamba a Lepu ndi dzuwa
Uploaded 4 years ago | Loading
9:53
Masamba sachedwa kuonongeka kotero zimakhala zovuta kuti anthu ogulitsa masamba ndi alimi agulitse. Koma pali njira zomwe alimi ndi ogulitsa masamba amachepetsa kuonongeka kwa masamba ngakhale nthawi yokolola itadutsa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Biovision Kenya, NASFAM Malawi, Egerton University Kenya, Sulma Foods Uganda