Kuthana ndi anakamfumbwe mu nthochi
Uploaded 3 years ago | Loading
11:30
Mu kanema uyu, tiphunzira momwe nakamfumbweyu amakulira, ndi kumudziwira komanso kufunika kogwiritsa ntchito mbeu yabwino poyamba munda watsopano wanthochi.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
NOGAMU