Ufulu wa alimi opeza mbewu: M'mene zithu zilili ku Malawi
Uploaded 7 years ago | Loading

13:54
Kuyambira make zana, alimi padziko lapansi ndi amene akhala oyang'anira mbewu ndi kuchulukitsa popanga mitundu ina yatsopano. Olemba ndondomeko amaona chinthu chovuta kulemekeza ufulu wa alimi posunga ndi kumalima mbewu chifukwa cha mbewu zopangidwa kufakitale. Koma alimi akuzindikira ufulu wawo ndikufunika kolima mbewu zawo.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight