Feteleza wamikodzo ya anthu
Uploaded 2 years ago | Loading
9:16
Ku dela Paya, nthaka ikupitilira kuguga chifukwa cholima mobwerezabwereza. Kanema uyu akuonetsa njira zomwe zikuthana ndi vutoli pogwiritsa ntchito feteleza wa mkodzo.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
LUND University, Sweden