Kulima bowa
Uploaded 4 years ago | Loading
11:55
Mukhoza kupeza ndalama zabwino ndithu ndi ulimi wabowa.Nthawi zonse mukhale aukhondo popeza chuku ndi majelemusi zikhoza kumera mukamadzala bowa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
KENAFF