Kuthana ndi matenda mu anyezi
Uploaded 1 year ago | Loading
10:00
Anyezi amakula bwino mu nyengo zosiyanasiyana, koma akalimidwa mu nyengo ya mvula, amagwidwa ndi matenda mosavuta. Anyezi akagwidwa ndi matenda, masamba amapindika ndipo izi zimachepetsa zokolora zanu. Matendawa amatha kuchokera mu dothi, ku nazale, komanso mbewu zotsalira mukakolora. Kanemayu akufotokozanso za mankwala ophera tizilombo m’mbewu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight