Kuthana ndi matenda a chiwawu mu tomato
Uploaded 3 years ago | Loading
8:51
Reference book
Chiwawu chimayamba chifukwa cha chuku chomwe chimakhala mnthaka komanso muzotsalila za mbewu. Chuku chimenechi ndicha mtundu wa fungus. Chimafala ndi tizilombo tosawoneka ndi maso.Pakuti nthendayi imafala mwachangu, Yendelani munda wanu tsiku lililonse. Mukapeza mbewu yamatenda, chotsani magawo a matendawo kuti asafalikire ku mbewu zina.Otchani mwachotsazo. Musasakanize ndi manyowa chifukwa matenda atha kupitilira kufalikila mmunda mwanu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action Nepal