Kupanga yoghurt ku Nyumba
Uploaded 8 years ago | Loading
11:52
Mu program iyi, tiphunzira mmene tingapangire yoghurt wabwino kunyumba. Mkaka ndichinthu chimodzi chofunika pokonza yoghurt, kotero muyenera kusamala posankha mkaka wabwino.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Egerton University