<<90000000>> viewers
<<240>> entrepreneurs in 17 countries
<<4135>> agroecology videos
<<105>> languages available

Kupanga rennet

Uploaded 3 years ago | Loading

Chofunika kwambiri popanga cheese ndi rennet. Izi zimangitsa mafuta mu mkaka kugwirana ndipo zotsala zinazo zimachoka. Pomwe mukhoza kugula rennet opangapanga wamadzi kapena ufa. Ku Egypt, amayi akumudzi amakonda kugwiritsa ntchito rennet kuchokera opezeka mmimba mwa kathole.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Nawaya
Share this video:
How you can help... Your generous donation will enable us to give smallholder farmers better access to agricultural advice in their language.

With thanks to our sponsors