Njira zachilengedwe zothanilana ndi kufufuma mimba kwa ziweto
Uploaded 2 years ago | Loading
12:34
Reference book
Kubvimbidwa kumachitika pomwe chiweto chadya msipu onyowa nthawi ya mvula. Mmimba mwachiweto, udzu onyowa umavundulana ndikupanga thovu. Komanso kumachitika pomwe mwasintha mwadzidzi chakudya chaziweto kapena kudya chipatso chakupsya kwambiri, masamba ang’ono-ang’ono a mapila koamanso masamba monga kabichi kapena cauliflower.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Atul Pagar, ANTHRA