<<90000000>> viewers
<<320>> entrepreneurs in 18 countries
<<5432>> agroecology videos
<<110>> languages available

Kuthana ndi Nthata kapena kuti nkhupakupa za ng’ombe

Uploaded 2 years ago | Loading

Nthata ndi tizilombo ting’onoting’ono timene timadziphatika ku ziweto kuti tiyamwe magazi. Ntahta zimenezi zimatha kuyambitsa matenda a zilonda zapakhundu. Zgiweto chimawonda ndipo chimatulutsa mkaka ochepa.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight
Share this video:

With thanks to our financial partners