Kusamalira mkaka kuti ukhale wabwino
Uploaded 2 years ago | Loading
12:00
Reference book
Makampani okonza mkaka amagula mkaka kuchokera kwa alimi ang’onoang’ono, kuti apangire zinthu zosiyansiyana. Makampanewa amalipira bwino koma pamafunika ukhondo, kotero amagula mkaka okwawo osamalika bwino.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight