Kusamalira Mphukira zamitengo mmunda
Uploaded 2 years ago | Loading

6:58
Reference book
Ntchito yosamalira mphukira za mitengo mminda yawo zathandizira kubwezeretsa mitengo malo okwana mahekitala five million ku Niger patadutsa zaka makumi atatu chilengedwe chitawonongeka. Iyi ndi njira yodalilika kumbali yobwenzeretsanso nkhalango za mmidzi ndi kulimbikitsa ulimi wa mitengo zomwe ndizothandizanso pa ulimi wa mbewu ndi ziweto.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Countrywise Communication, CIS Vrije Universiteit Amsterdam