Kuthana ndi matenda a chiwawu mu mpunga
Uploaded 4 years ago | Loading
12:49
Reference book
Mpunga ndi mbewu yofunikira mmayiko ambiri.Koma matenda osiyana-siyana atha kuwononga mbewu yanu.Amodzi mwamatenda osautsa ku mpunga ndi chiwawu amene amakonda kubwera kukakhala mphepo ya mkuntho.Pokha-pokha ngati mlimi atawa zindikira n’kuthana nawo mwachangu, matendawa atha kuwononga mpunga.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhai and Helvetas