Kupanga phala lopatsa thanzi posakaniza ndi juwisi wa malambe
Uploaded 2 years ago | Loading
07:53
Poyerekeza ndizakudya zina, phala la malambe lili ndi michere yambiri monga calcium, iron ndi magnesium komanso vitamin C. Kuwonjezera apo, lili ndi michere yothandiza kugaya zakudya mthupi. Phla lotere ndilabwino ku umoyo wa munthu poti limachepetsa chiopsezo chodwala dwala. Chifukwa cha michere yofunikirayi, zipatso za malambe zimatchedwa chakudya chapamwamba.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Hochschule Rhein-Waal, Biovision