Kupanga mphukira zathanzi za nthochi
Uploaded 2 years ago | Loading

13:55
Mmalo modzala mphukira yochokera ku thunthu, mutha kupanga mbewu yochuluka yatsopano, ya thanzi kuchokera ku phata la nthochi. Phunzirani momwe mungakonzekeretsere phata la nthcochi (pogwiritsa ntchito njira zachilengendwe) kuti mudzale mu utuchi panazale. Kuchokera kuphata limodzi liomdzi mutha kupezako mphukira zathanzi zopitilira 50 mu miyezi iwiri yokha.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Alcide Agbangla