kuthana ndi matenda a kuwola kwa kabichi
Uploaded 3 years ago | Loading
6:16
Alimi ambiri amasokoneza matendewa a kuwola kwa kabichi ndi matenda a nsabwe. Pamene matenda a nsabwe ndi atimadontho tamtundu wa purple, kuwola kwa kabichi amawoneka wachikasu komanso malo omwe wagwira amaoneka mwachilembo cha V.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Biovision