Kulima ndiwo zamasamba mu madimba oyandama pa madzi
Uploaded 2 years ago | Loading
14:15
Pomwe minda yathu yikukhala mmadzi osefukira nyengo ya mvula, makolo athu ankaganiza njira zolimira mbewu kuti tikhalebe ndi chakudya. Anapanga madimba oyandama pamadzi pogwiritsa ntchito zinyalala zotsalira ku mbewu. Sitimafunanso fetereza kapena mankhwala ophera tizirombo, chifukwa bedi loyandama limakhala ndimanyowa achilengedwe.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
CCDB