<<90000000>> viewers
<<240>> entrepreneurs in 17 countries
<<4135>> agroecology videos
<<105>> languages available

M’mene tingapewele mbozi mu mbewu zamasamba

Uploaded 7 years ago | Loading

Mbozi zimapezeka mu nthaka iliyonse ndipo ndichapafupi kuzipewa kusiyana ndi kuthana nazo zamoyo. Kuti tipewe mbozizi tikufunika kupanga izi: Tibzale mbewu zanthanzi, tichotse zonse zomwe zingapangitse kuti mbozi zipezeke mu munda wathu komanso malo oyandikana mdi munda wathu, tibzale mwakasithasitha ndi mbewu zomwe sizimagwidwa ndi mbozi, tipewe kubwelesa mbozi kuchokela minda zina pamunda pathu. Tiyeni tisanthule imodzi imodzi mwa njira zomwe tatchulazi. 

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight
Share this video:
How you can help... Your generous donation will enable us to give smallholder farmers better access to agricultural advice in their language.

With thanks to our sponsors