Ulimi wa ndiwo zamasamba kugwiritsa ntchito matumba
Uploaded 4 years ago | Loading
9:30
Aliyense akhoza kuzala mbeu zamasamba munthawi yochepa ndikuyamba kudya bwino komanso kupeza ndalama atagulitsa zotsala. Mu kanema uyu tiphunzira kuzala mbewu zamasamba mu dothi la mthumba.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
NOGAMU