Kukolola, kumenya ndi kusunga sesame
Uploaded 4 years ago | Loading
8:59
Reference book
Ulimi wa Sesame ndi wosavuta. Njira zoipa zokololera ndi kusunga zimasokoneza kaonekedwe kake. Miyala, mchenga ndi zinyalala zina zimasokoneza mtengo wa sesame.Mu kanema uyu, tiphunzira kukolola, kumenya ndi kusunga sesame kuti adzikhala wapamwamba.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Countrywise Communication