Kudzala chitowe mmizere ndi kuzulira
Uploaded 1 year ago | Loading
10:00
Reference book
Kudzala mmizere ndikopindulitsa chifukwa mumatha kuzulira mbeu zanu mosavuta. Ndipo nthambi zimachulukana. Mutha kuwerengera zitheba 20 pa nthambi iliyonse zomwe ndizochuluka kusiyana ndi kudzala mongowaza. Mbeu zikathinana, zimangokhala ndi chitheba chimodzi kapena ziwiri basi. Pazifukwa zonsezi ndikwabwino kudzala chitowe mmizere.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
MOBIOM