<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Njira zabwino zokololera chimanga

Uploaded 3 years ago | Loading

Mumadziwa kuti chimanga chanu chakhwima pamene masamba ndi makoko ayamba kuuma ndikusintha mtundu kupita ku chikasu, pamene bwenje wayamba kugwa pansi ndi, pamene chimanga chalimba.Sankhani tsiku lokololera. Yambani kukolola mbewu zamakono ndi kumalizira za lokolo zimene zimapilira ku matenda ndi tizirombo.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhai and Helvetas
Share this video:

With thanks to our sponsors