Kukokolola ndi kusunga njere zochokera ku mtengo wa shea
Uploaded 3 years ago | Loading
07:41
M’kanemayu tiphunzira m’mene tingatolere zipatso za shea, kuchotsa njere kuzipatsozi, kusankha, kuyanika, komanso kuswa, kuti mukhale ndi njere zabwino.Tiphunziranso m’mene tingasankhire, kuyanika ndikugireda njere za shea pokonzekera msika.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
NOGAMU, Sulma Foods Uganda