Kupanga mafuta apamwamba kuchokera ku shea
Uploaded 3 years ago | Loading
13:46
Mafuta a shea amagwiritsidwa ntchito kuphikira, kupangira mankhwala, komanso mafuta odzola. Mafutawa ndi njira yabwino yopezera ndalama kwa amai.Ukhondo ndi ofunikira pamene mukupanga mafuta a shea.Popanga mafuta a shea, pewani kugwiritsa ntchito zipangizo zina za chitsulo chifukwa zimatha kuwononga mafuta ndikubweretsa matenda.
Tsukani njere ndikuyanika padzuwa musanagayitse chifukwa njere zosaumitsitsa sizipereka mafuta ambiri.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AMEDD