<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Kupanga Feteleza watizilombo wamadzi komanso owuma ochokera ku manyowa

Uploaded 3 years ago | Loading

Kuti mukhale ndi mbewu zathanzi mukufunikira dothi la chonde. Dothili limakhala ndi tizilombo tofunikira ndi nyongolotsi. Kuti mukonze feteleza wa manyowa okwanira theka la hekitala, mufunikira zinthu izi;180 litres yamadzi oyera bwino;10 kg yandowe zaziwisi za ng’ombe;5 litres ya mkodzo wa ng’ombe;2 kg ya ufa wa tchana, kapena mbewu zina zamuguru la nyemba;1 kg ya zokometsera kapena shuga wa brown.dothi lodzadza Dzanja limodzi

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Atul Pagar, WOTR
Share this video:

With thanks to our sponsors