Kutonola, kusankha ndi kuyanika chimanga
Uploaded 4 years ago | Loading
14:54
Chimanga chitonoledwe, chipetedwe, chiyanikidwe komanso kusankha chisanapakilidwe.Tonolani pogwiritsa ntchito makina kapena pamanja. Yambani ndi kuyanika kuti chisateketeke kapena kuora.Chotsani zinyalara ndi fumbi popeta komaso posankha.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhai and Helvetas