Matenda a chiwawu mu chinangwa
Uploaded 4 years ago | Loading

11:39
Reference book
Matenda a chiwawu amachepetsa zokolola .Chizindikiro chimodzi cha nthendayi ndi madotho achikasu ndi obiriwira pang’ono pa masamba.Gulugufe ndiye amafalitsa nthendayi mu chinangwa.Nthendayi ilibe mankhwala koma ndi yopeweka.Tigwiritse ntchito mbeu yopanda matenda kuti tipewe matenda a chiwawu mu chinangwa. Ndibwino koposa kudzala mitundu ya mbeu yopilira ku matenda.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Songhaï Centre