Nsomba ngati chakudya, komanso chakudya cha nsomba
Uploaded 8 years ago | Loading
10:00
Mukanema uyu, tiphunzira mmene tingadyetsere nsomba zowetedwa mu dam. Choyamba, tiphunzira za Chakudya chansomba chopezekeratu mmadam. Kenaka tionanso mmene tingasamalire Chakudya chimenechi, Ndipo kumapeto tiona mmene tingaonjezere Chakudya mu dam lansomba.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight, Countrywise Communication, Digital Green, IRRI, NARC, Shushilan