Kuchita zinthu mogwirizana pofuna kuweta Nkhuku zathanzi
Uploaded 3 years ago | Loading
12:05
Mukanemayu, tipita mumzinda wa Fayoum, mdziko la Egypt, kumene gulu la amayi likuweta nkhuku poonetsetsa kuti ali ndi makola abwino, chakudya chofunikira, komanso dongosolo la katemera.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Nawaya, UNIDO Egypt