<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Kugonjetsa kaufiti podzula ndi manja

Uploaded 8 years ago | Loading

Khalani antcheru ndi kuonetsetsa ngati kaufiti ndi udzu wina zaphuka munda mwanu. Ndikofunika kuzula kafunika ndi manja nthawi yobeleka njele isanakwane komaso kufala ndikuononga mbewu.Mukanemayu timphuzira zifukwa zina kuonjezera kupalira udzu, kuti kuzula ndi manja kaufiti ndi kofunika kwambiri.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight, ICRISAT
Share this video:

With thanks to our sponsors