Kupanga cheese
Uploaded 4 years ago | Loading
12:51
Cheese chofewa chimatha kupangidwa kwa ola limodzi ndipo anthu akhoza kudya, chimapangidwa mosavuta pogwiritsa ntchito ziwiya zaku kitchen monga tiphunzilire kwa amayi a mmudzi mwa Sakkara ku Egypt.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Nawaya