Kuthandiza mai kuchira mwansanga akangochembeza
Uploaded 8 years ago | Loading
11:00
Mu kanema uyu tiphuzira mmene tingathandizire mai ongochira kumene: Kubwezera magazi nthupi, Kutsuka chibelekero ndi kuchepetsa ululu, kuzidalira komaso kukhala ndi chilakolako cha chakudya ndi kubwenzeretsa mphamvu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AMEDD