Manyowa amadzi: Chakudya chachilengedwe cha mbewu zanu
Uploaded 3 years ago | Loading
13:22
Reference book
Manyowawa ndi madzi amene mumapeza kuchokera kumanyowa opangidwa ndi nyongolotsi. Manyowawa amakhala ndi michere yamnthaka monga nitrogen, phosphorous ndi potassium, imene ndiyofunikira kwambiri ku mbewu zanu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Shanmuga Priya