Manyowa a kompoziti njira yogonjetsera kaufiti
Uploaded 7 years ago | Loading
10:14
Mukathira manyowa a kompoziti, chonde chimabwerera nthaka komaso imasunga chinyotho. Chithu chinaso chotsangalatsa ndichoti mumanyowa a kompoziti mumakhala tizilombo tomwe timalimbana ndi njele za kaufiti nthaka. Manyowa a kompoziti amachepetsa kuphukira kwa kaufiti ndipo izi zimathandiza kuchepetsa mavuto ku mbewu zagulu la mapila.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight, AMEDD, Countrywise Communication, FLASH, Fuma Gaskiya, ICRISAT, INRAN, UACT