<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Kasinthasintha Ndi Mbewu za mu Gulu la Nyemba

Uploaded 2 years ago | Loading

Mbewu zamguru lanyemba ndizabwino chifukwa zimabwenzeretsa chonde mthaka ndikugwirizana ndi tizilombo topanga nitrogen. Kuti nthaka yanu ikhale ndi tizilombo tokwanira mutha kugura Inokyulanti. Inokyulanti ali ndi tizilombo taphindu tomwe timakhala zakazingapo munthaka kotero simusowekera kuonjezera chaka chilichonse.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Nawaya
Share this video:

With thanks to our financial partners