Kuola kwa tsinde ndi mizu ya mtedza
Uploaded 3 years ago | Loading
13:10
Reference book
Ulimi wa Kasinthasintha, kuthira gypsum, zitsamba, komanso mafangasi ofunikira monga Trichoderma, atha kuthetsa vuto la matenda a kuwola kwa mizu komaso tsinde mu mbewu ya mtedza.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
MSSRF