Kukhala ndi mbeu yabwino ya thelele
Uploaded 4 years ago | Loading
12:16
Thelele limadzalidwa ndi thangala zokha. Koma ngati mudzala thangala zambiri pa zenje limodzi kapena mwadzala moyandikana, thelele limalephera kumera bwino. Mu kanema uyu alimi ku Benin ationetsa kadzalidwe koyenera ka thelele.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Alcide Agbangla