Kupanga ming’oma yamakono
Uploaded 4 years ago | Loading
15:30
Kudzera munjira yakale, njuchi zimapanga zokha malesa omwe amakhala ophatikana, kotero kukolola kumakhala kovuta. Munjira yamakono, uchi amapakula pogwiritsa ntchito chipangizo chopakulira uchi. Uchi umapakulidwa posaononga zitsa. Zisa zopanga kanthu amazibwenzeretsa kuti njuchi zikayikemo uchi wina, kotero kuthandiza njuchi kusataya nthawi ndi mphamvu kukonzanso kapena kubwenzeretsa zitsa.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action Nepal