Kusankha ndi kusunga maungu
Uploaded 3 years ago | Loading
9:15
Koma alimi amene amagulitsa maungu akangokolora, amagulitsa pa mtengo wotsika chifukwa amakhalapo ambiri pa msika.Atha kuwasunga kaye ndikudzagulitsa patsogolo akayamba kusowa, pamtengo wokwera.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Practical Action, Bangladesh and Nepal, Christian Commission for Development in Bangladesh (CCDB)