Kuthana ndi mbozi mu mbewu za masamba
Uploaded 3 years ago | Loading
10:49
Alimi aku Tamil Nadu, mdziko la India ationetsa mmene amathanirana ndi mbozi za mmasambazi. Njirayi itha kugwiranso m’zipatso.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
MSSRF