<<90000000>> viewers
<<320>> entrepreneurs in 18 countries
<<5432>> agroecology videos
<<110>> languages available

Kusunga Tomato wamphuphu komanso ofutsa

Uploaded 4 years ago | Loading

Mutha kusunga tomato mu mtsukowu kwa masabata awiri.Ikani tomato mu mtsuko waung’ono ndikukhazika mu waukulu wamabowo molekanitsa ndi mchenga.Thirani madzi mu mchenga kawiri patsiku kuti muziziritse tomato.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AMEDD
Share this video:

With thanks to our financial partners