Kusamalilra bwino tomato Nthawi Yokolora
Uploaded 3 years ago | Loading
6:30
Mukakolola tomato, pang’ono-pang’ono maonekedwe ake amayamba kusintha. Chomwe inu mungachite ndikuonetsetsa kuti mwamusamalira bwino kuti asaonongeke. Maonokedwe a tomato wabwino amayamba pokolola. Ngati mumugwire bwino ndiye kuti awonekanso bwino.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Countrywise Communication