Kuthana ndi matenda a tomato leaf curl virus
Uploaded 3 years ago | Loading
13:22
Mu kanema uyu, tiwona momwe tingathanirane ndi matendawa mu mabiringanya komanso mbewu zina.Matendawa amagwira mbewu nthawi iliyonse. Kachilimbo koyambitsa matendawa kamatha kukhalabe ndi moyo mu zotsalira za mbewu.Kachilomboka sikafa ndi mankhwala aliwonse.Kuti tithane ndi matendawa tikuyenera kudziwa momwe tingawazindikilire komanso momwe amafalikira.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
MSSRF