<<90000000>> viewers
<<240>> entrepreneurs in 17 countries
<<4135>> agroecology videos
<<105>> languages available

Kupanga bedi la manyowa a vermi-kompoziti

Uploaded 3 years ago | Loading

Gwiristani ntchito matumba akale a feteleza otsuka bwino, ndipo muwasoke kuti mupange bokosi. Yambani kuyala zinyalala zanu mmagawo ndikutsilira. Ikanimo nyongolosi pakatha sabata imodzi. Vindikililani ndi chiguguli ndikutsilira pafupi-pafupi. Onetsetsani kuti manyowa sali padzuwa.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
WOTR
Share this video:
How you can help... Your generous donation will enable us to give smallholder farmers better access to agricultural advice in their language.

With thanks to our sponsors