<<90000000>> viewers
<<320>> entrepreneurs in 18 countries
<<5432>> agroecology videos
<<110>> languages available

Ziwani za Udzu wa Kaufiti

Uploaded 8 years ago | Loading

Kaufiti ndi umodzi mwa udzu omwe umaononga mapila, nchewere ndi chimanga. Udzu odalira mbewu kuti ukule monga kaufiti, umapeza chakudya chake kuchokera kumbewu osati kunthaka. Mwakuti ntengo wa kaufiti umodzi umatha kubereka njere zokwana mazana angapo kapena zikwi zingapo. Njele zake ndi zazing’ono kwambiri moti alimi ambiri samazidziwa kuti ndi njele. Zimaoneka ngati dothi lakuda.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight, ICRISAT
Share this video:

With thanks to our financial partners