Kawokeledwe katsabola
Uploaded 8 years ago | Loading
11:35
Mbande zanthanzi ndi zopilila kumatenda ndi chiyambi cha mbewu ya tsabola yabwino. Kuti tichepetse chiwelengelo cha mbande zomwe zimafa powokela, tiyenela kusata njira zabwino: pamene tikukonzo nazale, pamene tikukonza dimba kapena munda wa mbewu zathu, komanso pamene tikuwokelambande zathu.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
Agro-Insight