Kubzala Nandolo mophatikiza ndi Chimanga
Uploaded 6 years ago | Loading
9:54
Mbewu monga nandolo, zimatenga Nayiturojini mumpweya ndikusunga m’dothi. Pamene nandolo wabzalidwa ndi mbewu zina, timibulu ta mizu yake timatulutsa mchere wa Nayiturojini. Mizu, masamba komanso mitengo ya nandolo yomwe yasiyidwa m’munda imathandiza kukonzanso nthaka.
Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
NASFAM