<<90000000>> viewers
<<266>> entrepreneurs in 18 countries
<<4647>> agroecology videos
<<107>> languages available

Kupanga Tomato Puree ndi juice kuchokera ku tomato

Uploaded 4 years ago | Loading

Nthawi zina tomato amasowa ndipo ogula amachita kugula tomato wa muchitini pa mtengo odula kufikira adzayambenso kupezeka. Komabe, pali njira zambiri zotherana ndi vutoli. Mukapanga tomato puree kuchokera ku tomato mukhoza kugwiritsa ntchito kwa chaka chimodzi ndipo juice kwa sabata imodzi kapena zitatu.

Current language
Chichewa / Nyanja
Produced by
AMEDD
Share this video:

With thanks to our financial partners